Yesaya 23:8 BL92

8 Ndani wapanga uphungu uno pa Turo, mudzi umene upereka akorona, amalonda ace ali akalonga, ogulitsa ace ali olemekezeka pa dziko lapansi?

Werengani mutu wathunthu Yesaya 23

Onani Yesaya 23:8 nkhani