Yesaya 24:22 BL92

22 Ndipo iwo adzasonkhanitsidwa pamodzi, monga ndende zimasonkhanitsidwa m'dzenje, ndi kutsekeredwa m'kaidi, ndipo atapita masiku ambiri adzawazonda.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 24

Onani Yesaya 24:22 nkhani