5 Dzikonso laipitsidwa ndi okhalamo ace omwe, cifukwa iwo alakwa pamalamulo nasinthanitsa malemba, natyola cipangano ca nthawi zonse.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 24
Onani Yesaya 24:5 nkhani