Yesaya 25:7 BL92

7 Ndipo Iye adzaononga m'phiri limeneli cophimba nkhope cobvundikira mitundu yonse ya anthu, ndi nsaru yokuta amitundu onse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 25

Onani Yesaya 25:7 nkhani