Yesaya 26:7 BL92

7 Njira ya wolungama iri njira yoongoka; Inu amene muli woongoka, mukonza njira ya wolungama.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 26

Onani Yesaya 26:7 nkhani