6 M'mibadwo ikudzayo Yakobo adzamera mizu; Israyeli adzaphuka ndi kucita mphundu; ndipo iwo adzadzaza ndi zipatso pa dziko lonse lapansi.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 27
Onani Yesaya 27:6 nkhani