22 Tsono musakhale amnyozo, kuti nsinga zanu zingalimbe; pakuti Ambuye, Yehova wa makamu, wandimvetsa za cionongeko cotsimikizidwa pa dziko lonse lapansi.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 28
Onani Yesaya 28:22 nkhani