25 Atakonza tyatyatya pamwamba pace, kodi safesa ponse mawere, ndi kumwazamwaza citowe, nafesa tirigu m'mizere ndi barele m'malo ace osankhika, ndi mcewere m'maliremo?
Werengani mutu wathunthu Yesaya 28
Onani Yesaya 28:25 nkhani