Yesaya 3:9 BL92

9 Maonekedwe a nkhope zao awacitira iwo mboni; ndipo amaonetsa ucimo wao monga Sodomu, saubisa. Tsoka kwa moyo wao! cifukwa iwo anadzicitira zoipa iwo okha.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 3

Onani Yesaya 3:9 nkhani