25 Ndipo pamwamba pa mapiri akuru onse, ndipa zitunda zonse zazitaritari padzakhala mitsinje ndi micerenje ya madzi, tsiku lophana lalikuru, pamene nsanja zidzagwa.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 30
Onani Yesaya 30:25 nkhani