Yesaya 30:3 BL92

3 Cifukwa cace mphamvu za Farao zidzakhala kwa inu manyazi, ndi kukhulupirira mthunzi wa Aigupto kudzakhala cisokonezo canu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 30

Onani Yesaya 30:3 nkhani