Yesaya 30:32 BL92

32 Ndipo nthawi zonse Yehova adze vakantha ndi ndodo yosankhikayo, padzamveka mangaka ndi zeze; ndi m'nkhondo zothunyana-thunyana, Iye adzamenyana nao.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 30

Onani Yesaya 30:32 nkhani