Yesaya 33:23 BL92

23 Zingwe zako za ngalawa zamasulidwa; sizinathe kulimbitsa patsinde pa mlongoti wace, sizinathe kufutukula matanga; pamenepo ndipo colanda cacikulu, cofunkha cinagawanidwa; wopunduka nafumfula.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 33

Onani Yesaya 33:23 nkhani