9 Dziko lilira maliro ndi kulefuka; Lebano ali ndi manyazi, nafota; Saroni afanana ndi cipululu; pa Basana ndi Karimeli papukutika.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 33
Onani Yesaya 33:9 nkhani