Yesaya 35:6 BL92

6 Pamenepo wopunduka adzatumpha ngati nswala, ndi lilume la wosalankhula lidzayimba; pakuti m'cipululu madzi adzaturuka, ndi mitsinje m'dziko loti se.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 35

Onani Yesaya 35:6 nkhani