Yesaya 36:11 BL92

11 Ndipo Eliakimu, ndi Sebina, ndi Yoaki, anati kwa kazembeyo, Nenanitu kwa atumiki anu m'cinenero ca Aramu; pakuti ife ticimva; ndipo musanene kwa ife m'Ciyuda, m'makutu a anthu amene ali palinga.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 36

Onani Yesaya 36:11 nkhani