16 Ambuye ndi zinthu izi anthu akhala ndi moyo.Ndipo m'menemo monse muli moyo wa mzimu wanga;Cifukwa cace mundiciritse ine,Ndi kundikhalitsa ndi moyo.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 38
Onani Yesaya 38:16 nkhani