Yesaya 38:20 BL92

20 Yehova ndiye wondipulumutsa ine;Cifukwa cace tidzayimba nyimbo zanga, ndi zoyimba zazingweMasiku onse a moyo wathu m'nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 38

Onani Yesaya 38:20 nkhani