Yesaya 38:3 BL92

3 Kumbukiranitu tsopano, Yehova, kuti ndayenda pamaso panu m'zoonadi ndi mtima wangwiro, ndipo ndacita zabwino pamaso panu. Ndipo Hezekiya analira kolimba.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 38

Onani Yesaya 38:3 nkhani