8 Ndipo Hezekiya anati kwa Yesaya, Mau a Yehova, amene iwe wanena, ali abwino. Iye anatinso, Pakuti padzakhala mtendere ndi zoonadi masiku anga.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 39
Onani Yesaya 39:8 nkhani