Yesaya 40:11 BL92

11 Iye adzadyetsa zoweta zace ngati mbusa, nadzasonkhanitsa ana a nkhosa pacapa pace, nadzawatengera pa cifuwa cace, ndipo adzatsogolera bwino bwino zimene ziyamwitsa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 40

Onani Yesaya 40:11 nkhani