24 Inde sanaokedwe, inde sanafesedwe; inde, muzu wao sunazike pansi; koma Iye anawaombetsera mphepo, ndipo afota, ndipo kabvumvulu awacotsa monga ciputu.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 40
Onani Yesaya 40:24 nkhani