Yesaya 40:28 BL92

28 Kodi iwe sunadziwe? kodi sunamve? Mulungu wacikhalire, Yehova, Mlengi wa malekezero a dziko lapansi, salefuka konse, salema; nzeru zace sizisanthulika.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 40

Onani Yesaya 40:28 nkhani