Yesaya 41:23 BL92

23 Chulani zinthu zimene zirinkudza m'tsogolo, kuti ife tidziwe kuti inu ndinu milungu; inde, citani zabwino, kapena citani zoipa, kuti ife tiopsyedwe, ndi kuona pamodzi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 41

Onani Yesaya 41:23 nkhani