Yesaya 41:28 BL92

28 Ndipo pamene ndayang'ana, palibe munthu; ngakhale mwa iwo, palibe phungu, amene angathe kuyankha mau, pamene ndiwafunsa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 41

Onani Yesaya 41:28 nkhani