Yesaya 41:4 BL92

4 Ndani wacipanga, nacimariza ico, kuchula mibadwo ciyambire? Ine Yehova, ndine woyamba, ndi pacimariziro ndine ndemwe.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 41

Onani Yesaya 41:4 nkhani