Yesaya 42:14 BL92

14 Ndakhala nthawi yambiri wosalankhula; ndakhala cete ndi kudzithungata ndekha; tsopano ndidzapfuula ngati mkazi wobala; ndidzapuma modukizadukiza ndi wefuwefu pamodzi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 42

Onani Yesaya 42:14 nkhani