Yesaya 42:4 BL92

4 Iye sadzalephera kapena kudololoka, kufikira atakhazikitsa ciweruzo m'dziko lapansi; ndipo zisumbu zidzalindira cilamulo cace.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 42

Onani Yesaya 42:4 nkhani