Yesaya 43:19 BL92

19 Taonani, ine ndidzacita cinthu catsopano; tsopano cidzaoneka; kodi simudzacidziwa? Ndidzakonzadi njira m'cipululu, ndi mitsinje m'zidalala.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 43

Onani Yesaya 43:19 nkhani