Yesaya 46:6 BL92

6 Amene ataya golidi, namturutsa m'thumba, ndi kuyesa siliva ndi muyeso, iwo alemba wosula golidi; iye napanga nazo mlungu; iwo agwada pansi, inde alambira.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 46

Onani Yesaya 46:6 nkhani