13 Inde dzanja langa linakhazika maziko a dziko lapansi, ndi dzanja langa lamanja linafunyulula m'mwamba; pakuziitana Ine ziimirira pamodzi.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 48
Onani Yesaya 48:13 nkhani