Yesaya 5:13 BL92

13 Cifukwa cace anthu anga amuka m'nsinga, cifukwa ca kusowa nzeru; ndi amuna ao olemekezeka ali ndi njala, ndi khamu lao lauma kukhosi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 5

Onani Yesaya 5:13 nkhani