Yesaya 5:17 BL92

17 Pamenepo ana a nkhosa adzadyapo ngati m'busa mwao, ndi malo a bwinja a zonenepa zacilendo zidzadyapo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 5

Onani Yesaya 5:17 nkhani