Yesaya 5:26 BL92

26 Ndipo Iye adzakwezera a mitundu yakutari mbendera, nadzawayimbira mluzu, acokere ku malekezero a dziko; ndipo taonani, iwo adzadza ndi liwiro msanga msanga;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 5

Onani Yesaya 5:26 nkhani