Yesaya 5:8 BL92

8 Tsoka kwa iwo amene aphatikiza nyumba ndi nyumba, amene alumikiza munda ndi munda, kufikira padzapanda malo, ndipo inu mudzasiyidwa nokha pakati pa dziko!

Werengani mutu wathunthu Yesaya 5

Onani Yesaya 5:8 nkhani