6 Ndinapereka msana wanga kwa omenya, ndi masaya anga kwa iwo amene anakudzula tsitsi langa; sindinabisira nkhope yanga manyazi ndi kulabvulidwa.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 50
Onani Yesaya 50:6 nkhani