8 Iye ali pafupi amene alungamitsa Ine; ndani adzakangana ndi Ine? tiyeni tiimirire tonse pamodzi; mdani wanga ndani? andiyandikire.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 50
Onani Yesaya 50:8 nkhani