Yesaya 51:12 BL92

12 Ine, Inedi, ndine amene nditonthoza mtima wako; kodi iwe ndani, kuti uopa munthu amene adzafa, ndi mwana wa munthu amene adzakhala ngati udzu;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 51

Onani Yesaya 51:12 nkhani