Yesaya 51:2 BL92

2 Yang'anani kwa Abrahamu kholo lanu, ndi kwa Sara amene anakubalani inu; pakuti pamene iye anali mmodzi yekha ndinamuitana iye; ndipo ndinamdalitsa ndi kumcurukitsa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 51

Onani Yesaya 51:2 nkhani