4 Zoonadi Iye ananyamula zowawa zathu, ndi kusenza zisoni zathu; koma ife tinamuvesa wokhomedwa wokanthidwa ndi Mulungu, ndi wobvutidwa.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 53
Onani Yesaya 53:4 nkhani