9 Ndipo anaika manda ace pamodzi ndi oipa, ndi pamodzi ndi olemera mu imfa yace, ngakhale Iye sanacita ciwawa, ndipo m'kamwa mwace munalibe cinyengo.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 53
Onani Yesaya 53:9 nkhani