14 M'cilungamo iwe udzakhazikitsidwa, udzakhala kutari ndi cipsinjo, pakuti sudzaopa; udzakhala kutari ndi mantha, pakuti sadzafika cifupi ndi iwe.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 54
Onani Yesaya 54:14 nkhani