8 M'kukwiya kwa kusefukira ndinakubisira nkhope yanga kamphindi; koma ndi kukoma mtima kwa cikhalire ndidzakucitira cifundo, ati Yehova Mombolo wako.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 54
Onani Yesaya 54:8 nkhani