Yesaya 55:10 BL92

10 Pakuti monga mvula imagwa pansi ndi matalala, kucokera kumwamba yosabwerera komweko, koma ikhamiza nthaka ndi kuibalitsa, ndi kuiphukitsa, ndi kuipatsitsa mbeu kwa wobzyala, ndi cakudya kwa wakudya;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 55

Onani Yesaya 55:10 nkhani