Yesaya 55:12 BL92

12 Pakuti inu mudzaturuka ndi kukondwa, ndi kutsogozedwa ndi mtendere; mapiri ndi zitunda, zidzayimba zolimba pamaso panu, ndi mitengo yonse ya m'thengo idzaomba m'manja mwao.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 55

Onani Yesaya 55:12 nkhani