Yesaya 56:2 BL92

2 Wodala munthu amene acita ici, ndi mwana wa munthu amene agwira zolimba ici, amene asunga sabata osaliipitsa, nasunga dzanja lace osacita nalo coipa ciri conse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 56

Onani Yesaya 56:2 nkhani