5 Kwa iyo ndidzapatsa m'nyumba yanga ndi m'kati mwa makoma anga malo, ndi dzina loposa la ana amuna ndi akazi; ndidzawapatsa dzina lacikhalire limene silidzadulidwa.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 56
Onani Yesaya 56:5 nkhani