Yesaya 57:5 BL92

5 Inu amene muutsa zilakolako zanu pakati pa mathundu, patsinde pa mitengo yonse ya gudugudu, amene mupha ana m'zigwa pansi pa mapanga a matanthwe?

Werengani mutu wathunthu Yesaya 57

Onani Yesaya 57:5 nkhani