12 Ndipo iwo amene adzakhala a iwe adzamanga malo akale abwinja; udzautsa maziko a mibadwo yambiri; udzachedwa Wokonza pogumuka, Wakubwezera njira zakukhalamo.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 58
Onani Yesaya 58:12 nkhani