Yesaya 58:4 BL92

4 Taonani, inu musala kudya kuti mukangane ndi kutsutsana ndi kukantha ndi nkhonya yoipa; inu simusala kudya tsiku lalero kuti mumveketse mau anu kumwamba.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 58

Onani Yesaya 58:4 nkhani